Kodi Deriv Bot ndi chiyani?
Deriv Bot ndi chida chomangira njira za malonda pa intaneti kuti muzichita malonda a digital options. Ndi pulatifomu yomwe mumatha kupangira bot yanu ya malonda pogwiritsa ntchito 'ma blocks' omwe mumakoka ndi kuika (drag-and-drop).






