Kodi ndingasunge bwanji njira yanga pa Deriv Bot?
Mu Bot Builder, dinani Save pa msera wazida womwe uli pamwamba kuti mutsitse bot yanu. Perekani dzina ku bot yanu, ndipo sankhani kutsitsa bot yanu ku chipangizo chanu kapena ku Google Drive. Bot yanu idzatsitsidwa ngati fayilo ya XML.






