Kodi quick strategy ndi chiyani?
Quick strategy ndi njira yokonzeka kale imene mungagwiritse ntchito mu Deriv Bot. Pali ma quick strategy 3 amene mungasankhepo: Martingale, D'Alembert, ndi Oscar's Grind.
Kugwiritsa ntchito quick strategy
- Pitani ku Quick strategy ndipo sankhani njira imene mukufuna.
- Sankhani asset ndi mtundu wa malonda.
- Ikani ma parameter a malonda anu kenako dinani Create.
- Ma block akangoloŵa mu workspace, mukhoza kusintha ma parameter ngati mukufuna, kapena dinani Run kuti muyambe malonda.
- Dinani Save kuti mutsitse bot yanu. Mungasankhe kutsitsira bot yanu pa chipangizo chanu kapena pa Google Drive yanu.






