Skip to main content

Deriv MT5 signals

Utumiki wa MT5 trading signals umakulolani kulembetsa ndikutsanzira malonda a amalonda odziwa zambiri, kapena kupatsira amalonda ena njira zanu poyika ndalama zochita subscription.

Tsanzirani malonda a akatswiri mwaokha mu akaunti yanu ya Deriv MT5, kaya kwaulere kapena polipira. Mukalembetsa signal ya malonda, malonda a provider amatsanziridwa mwaokha mu akaunti yanu ya malonda ya Deriv MT5 nthawi iliyonse yomwe achita malonda.

Ubwino wa kulembetsa ma MT5 trading signals

Malonda ochokera kwa amalonda odziwa bwino amatsanziridwa mwaokha mu akaunti yanu.

Sungani nthawi – kulembetsa ma signals kumapangitsa malonda anu kukhala oyendetsedwa mwaokha.

Zosavuta kukhazikitsa – palibe kufunika kuyika chinthu chilichonse.

Chidziwitso chonse cha momwe provider aliyense wagwirira ntchito.

Palibe ndalama zobisika kapena ma commission.

Mmene mungalembetsere signal ya MT5 trading

Sitepu 1

Pitani ku MQL5 Signals

Mu MT5 trading terminal yanu, pitani ku Tools ndikusankha MQL5 Signals.

Pitani ku MQL5 Signals

Sitepu 2

Lembetsani signal provider

Sankhani signal provider yomwe mukufuna ndikudina “Subscribe”.

Lembetsani signal provider

Sitepu 3

Malizani kulembetsa kwanu

Sinthani zoyendetsera malonda anu ndi kuwongolera chiwopsezo. Kenako dinani “OK” kuti mumalize kulembetsa.

Malizani kulembetsa kwanu

Mmene mungakonzenso kapena kuletsa kulembetsa kwanu

Sitepu 1

Pitani ku My Statistics

Mu Navigator panel, pitani ku Signals ndikudina “My Statistics”.

Pitani ku My Statistics

Sitepu 2

Sankhani provider

Sankhani signal provider yomwe mukufuna kukonzanso kapena kuletsa kulembetsa kwanu.

Sankhani provider

Sitepu 3

Konzanso kapena letsani kulembetsa

Dinani “Renew” kapena “Unsubscribe” kuti mukonzenso kapena muletse kulembetsa kwanu.

Konzanso kapena letsani kulembetsa

Note:

  1. Mufunika akaunti ya MQL5 community kuti mulembetse ma trading signals. Ngati mulibe akaunti, pitani ku MQL5.com kuti mukalembetse.
  2. Kuti mulembetse ma signals olipiritsa, ikani ndalama mu akaunti yanu ya MQL5.
  3. Mutha kulembetsa signal provider m'modzi kokha ndi akaunti imodzi ya Deriv MT5 pa nthawi ina iliyonse. Mutha kugwiritsa ntchito signal yanu pa makompyuta osiyana osiyana mpaka atatu.
  4. Mukangolembetsa signal, simudzatha kuchita malonda mwanokha ndi akaunti yomweyo ya Deriv MT5.

Mafunso anu ayankhidwa

Izi zimatengera signal provider yomwe mukulembetsa nayo ndi mtengo wa subscription womwe wakhazikitsidwa.
Musanalembetse signal provider, onani zinthu monga mbiri yawo yakale, njira yawo yamalonda, ndi chiwopsezo chake. Funafunani provider amene amagwirizana ndi kupirira kwanu chiwopsezo ndi zolinga zanu za malonda.

Lowani nawo Amalonda
oposa 3M padziko lonse

Tsegulani akaunti pasanathe mphindi zochepa ndikuyamba kuchita malonda pa misika ya padziko lonse — forex, masheya, ziwerengero za masheya, ndi zina.

WhatsApp