N'chifukwa chiyani mutisankhe
Kwa zaka zoposa 25, Deriv wakhala mnzake wodalirika wa amalonda padziko lonse lapansi. Timanyadira njira yathu yoyang'ana makasitomala poyamba, kuonetsetsa kuti zofuna zawo nthawi zonse zikhala patsogolo. Mbiri yathu yodalirika pa malonda oyang'aniridwa, kuphatikiza ndi chitetezo cholimba cha ndalama za makasitomala, zimatipangitsa kukhala chisankho chodziwikiratu kwa amalonda.
Mphotho zathu
Best Trade Execution Award (MEA)
Ultimate Fintech 2026
Best Trading Experience - Global
UF Awards 2025
Best CFD Broker - LATAM
UF Awards 2025
Most Innovative Broker - MEA
UF Awards 2025
Most Transparent Broker - Global
Global Forex Awards 2025
Best Broker - Africa
Global Forex Awards 2025
Best Trading Platform - MENA
Global Forex Awards 2025
Most Innovative Online Trading Platform
Forex Expo Dubai 2025
Chief Risk & Compliance Officer of the Year
Forex Expo Dubai 2025
Best Broker - APAC
UF Awards 2025
Best Trading Conditions - Global
Finance Magnates 2025
Most Trusted Broker - Middle East
Finance Magnates 2025
Affiliate Program of the Year
Forex Expo Dubai 2024
Best Customer Service - Global
Global Forex Awards 2024
Most Trusted Broker - Africa
Finance Magnates 2024
Best LATAM Region Broker
ADVFN Awards 2024
Broker of the Year - Global

Mbiri yodalirika
Gulu la Deriv lili ndi mbiri yakale yomwe idayamba mu 1999 pamene tidayika maziko a ntchito yoyamba padziko lonse ya malonda a fixed-odds. Kuchokera pamenepo, takula ndikupitirira, kupeza chidaliro cha amalonda padziko lonse lapansi.
Chitetezo cha ndalama za makasitomala
Deriv sagwiritsa ntchito ndalama zanu pa zofuna zake zamabizinesi ndipo mumaloledwa kutulutsa ndalama zanu nthawi iliyonse. Ndalama zanu zonse zimasungidwa padera m'mabungwe azachuma. Motero, ngati Deriv atangokhala wosakhoza kulipira (chinthu chomwe n'chosachitika kaŵirikaŵiri), ndalama zanu zonse zidzabwezedwa kwa inu chifukwa sizisakanikirana ndi zathu.
Kuzindikira ndi kuyang'anira ziwopsezo
Malonda pa intaneti ndi osangalatsa koma amakhala ndi ziwopsezo ndipo angayambitse kudzikakamiza kwambiri. Pa Deriv, timayang'ana zofuna zabwino za makasitomala athu ndipo timawalimbikitsa kuchita malonda otetezeka komanso mwaudindo. Ngati muli achatsopano pa izi, mungathenso kuyeserera malonda ndi ndalama zochita-nazo (virtual funds) zosaŵerengeka musanaike pa chiwopsezo ndalama zanu.
Dziwani zambiri: Kuzindikira ndi kuyang'anira ziwopsezoThandizo pamene mukulifuna
Gulu la thandizo la Deriv limapezeka kudzera pa live chat 24/7 – ngakhale pa sabata ndi weekend. Mungathenso kupeza mayankho ku help centre yathu ndikupeza thandizo kuchokera kwa amalonda anzanu mu Community.
Dziwani zambiri: Thandizo pamene mukulifunaMalonda oyang'ana kasitomala poyamba
Deriv imapangitsa kukhala kophweka kwa aliyense kuyamba malonda, kumvetsetsa chiwopsezo, ndi kupanga zisankho zabwino za malonda. Zida ndi mapulatifomu athu ali ndi malangizo omveka bwino komanso osavuta ndipo ndi ophweka kuyenda nawo. Timaperekanso nthawi ndi nthawi nkhani za msika, kusanthula, ma webinar, mabuku a ebook, ma video oyendetsera, ndi nkhani za help centre kuti tikuthandizeni kukhala odziwa zambiri ndi kukhala wamalonda wabwinoko.

Zomwe makasitomala athu amanena
Chitani malonda mopanda chiwopsezo pogwiritsa ntchito akaunti ya demo
Ndalama Zochita-nazo Zosaŵerengeka
Yeserani malonda ndi Deriv kwa nthawi yaitali monga mukufunira. Palibe chiwopsezo, palibe malipiro obisika.
Misika ndi mapulatifomu onse
Sangalalani ndi mwayi wathunthu wolowa m'misika ndi mapulatifomu athu onse.
Palibe kadi ya credit yofunika
Lembetsani pogwiritsa ntchito imelo yanu yokha. Palibe kadi ya credit kapena ndalama zochepa zoyenera kuyika.