Kodi Chikwatu n'chiyani?
Chikwatu ndi malo anu apakati oyang'anirira ndalama mkati mwa Deriv. Mutha kuika, kusunga, kutumiza, ndi kutulutsa ndalama pogwiritsa ntchito Chikwatu chanu. Mudzatha kuika ndalama mu Chikwatu chanu mu USD kapena ndalama ya crypto yomwe mumakonda.






