Kodi pali malipiro aliwonse pa kuyika kapena kutulutsa ndalama pa Deriv?
Palibe malipiro pa kuyika ndalama mu Deriv Wallet yanu. Kwa kutulutsa ndalama, njira ya kulipirira yomwe mwasankha ingakhometse malipiro a kutulutsa ndalama. Izi zidzatengera njira ya kutulutsa ndalama yomwe mwasankha.






