Kodi ndingadziteteze bwanji ku zinyengo za umboni wolipira pa Deriv P2P?
Anthu ochita zachinyengo amatha kutumiza zithunzi zabodza za pomwe pawakidwa ndalama kuti akukakamizeni kuchitapo kanthu.
Zomwe muyenera kuchita
Nthawi zonse onetsetsani ndi banki yanu kapena e-wallet yanu musanamasule ndalama.






