Ndingasinthe bwanji password yanga ya Deriv MT5?
Tsatirani njira izi kuti mukonzenso password yanu ya Deriv MT5:
1. Pitani ku akaunti yanu ya Deriv MT5.
2. Dinani Details.
3. Dinani Forgot password. Mudzafunsidwa kuti mulowetse password yatsopano ya akaunti yanu ya Deriv MT5.
4. Tidzatumiza verification code ku imelo yanu. Lowetsani verification code kuti mutsimikizire kukonzanso kwa password.
5. Muwona sikirini yotsimikizira kuti kukonzanso password kwachitika bwino.
Tsopano mutha kulowa mu Deriv MT5 pogwiritsa ntchito password yanu yatsopano.






