Chifukwa chochitira malonda a Vanilla Options pa Deriv
Sankhani milingo yanu ya strike
Chitani malonda pa mamalo a mtengo omwe akugwirizana ndi kusanthula kwanu kwa msika — pamtengo womwewo, pamwamba, kapena pansi pa mtengo wapano.

Chiwopsezo choyang'aniridwa
Ikani stake yanu ndipo onani zomwe mungapeze pasadakhale.

Kusintha mogwirizana ndi msika
Chitani malonda m'mikhalidwe yosiyanasiyana ya msika kuti igwirizane ndi njira yanu.

Mmene Vanilla Options zimagwirira ntchito
Sankhani strike price ndipo gangani za udindo wanu. Tsegulani udindo wa Call ngati mukuyembekezera mtengo kukwera pamwamba pa strike price, kapena udindo wa Put ngati mukuganiza kuti utsikira pansi pake. Ndi nthawi zokhazikika za expiry, izi zimapereka malonda olondola pa milingo ya mtengo.
Mayankho a mafunso anu
Mungakondenso izi
Digital Options
Neneratu zotsatira ndipo pezani payout yokhazikika ngati kuneneratu kwanu ndi kolondola.
Dziwani zambiriAccumulators
Kulitsani phindu lanu lotheka ndi kukula kwa compounding mpaka 5% pa tick.
Dziwani zambiriTurbos
Pezani payout ngati kuneneratu kwanu ndi kolondola ndipo mtengo ukhalabe pakati pa mpanda wokhazikitsidwa.
Dziwani zambiriMultipliers
Onjezani phindu lanu lotheka mpaka 2,000x ngati msika usuntha mmene mukufunira.
Dziwani zambiri