Chifukwa chochitira malonda a Accumulator Options pa Deriv
Chitani malonda pamene ena akudikira
Chitani malonda m'misika yokhazikika pamene mitengo ikusintha mkati mwa gawo lofanana.

Tulukani nthawi iliyonse
Yang'anirani nthawi ya positsiyoni yanu — kuyambira tick yoyamba mpaka kutha.

Chitani malonda ndi chiwopsezo chodziwika
Ndi chiwopsezo chodziwika kale, mumadziwa nthawi zonse ndalama zomwe mungataye musanachite malonda.

Mmene Accumulator Options amagwirira ntchito
Sankhani chiwongoladzanja cha kukula pakati pa 1–5% ndipo onani ngati mtengo wa msika ukhala mkati mwa gawo lodziwika kuchokera pa mtengo wa spot wapitawo. Payout yanu imakula mwachangu (exponentially) malinga ndi chiwongoladzanja cha kukula chomwe musankha. Kumbukirani: chiwongoladzanja chachikulu cha kukula chimatanthauza magawo opapatiza a kusintha kwa mtengo.
Mafunso anu ayankhidwa
Mungakondwenso ndi izi
Digital Options
Neneratu zomwe zichitike ndipo mupeze payout yokhazikika ngati kuneneratu kwanu ndi kolondola.
Dziwani zambiriVanillas
Landani payout yayikulu ngati maneneratu anu ndi olondola mkati mwa nthawi ya pangano.
Dziwani zambiriTurbos
Landani payout ngati kuneneratu kwanu ndi kolondola ndipo mtengo ukhala mkati mwa mzere wodziwika (barrier).
Dziwani zambiriMultipliers
Kulitsani phindu lanu lomwe mungapeze mpaka nthawi 2,000 ngati msika usintha mmokomera inu.
Dziwani zambiri