Vanillas
Landirani Payout yayikulu ngati maganizo anu olondola ali mkati mwa nthawi ya kontrakiti.
Chitani Malonda a VanillasKodi mungachite bwanji malonda a Vanillas?
Vanillas zimakulolani kuti muneneratu ngati mtengo wa chinthu choyambira (underlying asset) udzakhala pamwamba kapena pansi pa strike price pamene kontrakiti ikutha (exit spot).
Call
Landirani Payout ngati exit spot ili pamwamba pa strike price pamene kontrakiti ikutha.
Put
Landirani Payout ngati exit spot ili pansi pa strike price pamene kontrakiti ikutha.
Zambiri zowonjezera
Mumapeza phindu pokhapokha ngati Payout ili yayikulu kuposa Stake yanu.
Mutha kugulitsa kontrakiti yanu mpaka masekondi 60 kontrakiti isanathe. Mukatero, tidzakulipirani mtengo wa kontrakiti.