Turbos
Landilani payout ngati kuneneratu kwanu ndi kolondola ndipo mtengo ukhalabe mkati mwa malire oikidwa.
Chitani Malonda a TurbosKodi mumachita bwanji malonda a Turbos?
Turbos zimakulolani kuneneratu mmene chinthu chomwe malondawo akuchokera chidzasunthira.
Kukwera
Landilani payout ngati mtengo wa spot supitirira pansi pa malire munthawi yonse ya kontrakiti.
Kutsika
Landilani payout ngati mtengo wa spot supitirira pamwamba pa malire munthawi yonse ya kontrakiti.
Zambiri zowonjezera
Ngati malirewo aphwanyidwa nthawi iliyonse, kontrakiti yanu imatha msanga.
Mumapeza phindu pokhapokha ngati payout yanu ndi yayikulu kuposa stake yanu.
Mutha kugulitsa kontrakiti yanu masekondi 15 asanafike nthawi yoti ithe. Mukatero, tidzakulipirani mtengo wa kontrakiti.
Ngati mwaika nthawi yanu mu ticks, simungathe kutseka kontrakiti musanafike nthawi yake.