Higher/Lower
Chitani Malonda a Higher/LowerKodi mungachite bwanji malonda a Higher/Lower?
Higher
Landirani payout ngati exit spot ili pamwamba kwenikweni pa barrier.
Lower
Landirani payout ngati exit spot ili pansi kwenikweni pa barrier.
Zambiri Zowonjezera
Ngati exit spot ili yofanana ndi barrier, simulandira payout.