Malonda a Options
Mapangano a Options amakulolani kulingalira za kayendedwe ka msika pazinthu zosiyanasiyana zachuma ndi Derived Indices.
Mitundu ya Options
Vanillas
Pezani payout yayikulu ngati zoneneratu zanu n'zolondola pasanathe nthawi ya pangano.
Dziwani zambiri
Accumulators
Onjezerani phindu limene mungapeze ndi kukula kwa mpaka 5% pa tick iliyonse.
Dziwani zambiri
Turbos
Pezani payout ngati chineneratu chanu n'cholondola ndipo mtengo wakhala mkati mwa malire oikidwa.
Dziwani zambiri
Multipliers
Onjezerani phindu limene mungapeze mpaka nthawi 4,000 ngati msika wayenda mmene mukufunira.
Dziwani zambiri
Digital Options
Neneratu zotsatira ndipo pezani payout yokhazikika ngati chineneratu chanu n'cholondola.
Dziwani zambiri
Chifukwa chochitira malonda a Options pa Deriv
Mapangano osinthasintha
Sankhani pakati pa mitundu yosiyanasiyana ya mapangano ndi nthawi zake kuti zigwirizane ndi njira yanu yamalonda.
Mtengo wocheperapo woyambira
Yambani malonda ndi ndalama zochepa ngati USD 1, ndi mtengo wocheperapo wa USD 5 mu akaunti yanu.
Ma payout osinthasintha
Pezani payout yayikulu ngati zoneneratu zanu n'zolondola pasanathe nthawi ya pangano.