Digital Options
Neneraniratu momwe mtengo wa msika udzasinthire ndipo mupeze Payout yokhazikika mukanena molondola. Chiwopsezo chimakhala chochepetsedwa ku ndalama yanu yoyambirira.
Kodi Digital Options zimagwira ntchito bwanji?
Neneraniratu momwe mtengo wa chinthu (asset) udzasinthire mkati mwa nthawi ndi mkhalidwe wapadera. Ngati chomwe mwanenera nchoona, mudzalandira Payout yokhazikika. Ngati sichoona, kutayika kwanu kumakhala kochepetsedwa ku ndalama imene munagwiritsa ntchito pomalonda.